Acts 18:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma popeza kuti ndi nkhani yokhudza mau, ndi maina, ndiponso Malamulo anu, mudziwonere nokha. Kuti ndiweruze zimenezi, ine toto.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma akakhala mafunso a mau ndi maina ndi chilamulo chanu; muyang'ane inu nokha; sindifuna kuweruza zimenezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma popeza ndi nkhani yokhudza mawu, mayina ndi malamulo anu, kambiranani nokhanokha. Ine sindidzaweruza zinthu zimenezi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma akakhala mafunso a mau ndi maina ndi cilamulo canu; muyang'ane inu nokha; sindifuna kuweruza zimenezi.