Acts 18:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵatsazika naŵauza kuti, “Mulungu akalola ndidzabweranso.” Atatero adachoka ku Efeso m'chombo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma anawatsanzika, nati, Akafuna Mulungu, ndidzabwera kwa inu; ndipo anachoka ku Efeso m'ngalawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene amachoka anawalonjeza kuti, “Ndidzabweranso Mulungu akalola.” Ndipo anakwera sitima ya pamadzi kuchoka ku Efeso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma anawatsazika, nati, Akafuna Mulungu, ndidzabwera kwa inu; ndipo anacoka ku Efeso m'ngalawa.