Acts 18:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atakhala kumeneko kanthaŵi ndithu, adachokako nakayendera dziko la Galatiya ndi la Frijiya, akulimbikitsa ophunzira onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atakhala kumeneko nthawi, anachoka, napita ku madera osiyanasiyana a dziko la Galatiya ndi la Frijiya, nakhazikitsa ophunzira onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atakhala kwa kanthawi ku Antiokeya, Paulo anachokako nayendera madera onse a ku Galatiya ndi ku Frugiya kulimbikitsa ophunzira onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atakhala kumeneko nthawi, anacoka, napita pa dziko la Galatiya ndi Frugiya m'dziko m'dziko, nakhazikitsaakuphunzira onse.