Acts 18:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Myuda wina, dzina lake Apolo, mbadwa ya ku Aleksandriya, adabwera ku Efeso. Anali munthu wodziŵa kulankhula ndi wodziŵa Malembo kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anafika ku Efeso Myuda wina dzina lake Apolo, fuko lake la ku Aleksandriya, munthu wolankhula mwanzeru; ndipo anali wamphamvu m'malembo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi yomweyi Myuda wina dzina lake Apolo, mbadwa ya ku Alekisandriya anafika ku Efeso. Anali munthu wophunzira ndi wodziwa bwino Malemba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anafika ku Efeso Myuda wina dzina lace Apolo, pfuko lace la ku Alesandreya, munthu wolankhula mwanzeru; ndipo anali wamphamvu m'malembo.