Acts 19:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paulo adaafuna kuloŵa pakati pa anthuwo, koma ophunzira sadamloleze.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Paulo anafuna kulowa kwa anthu, ophunzira ake sanamloleza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo anafuna kulowa pakati pa gulu la anthu, koma ophunzira anamuletsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Paulo anafuna kulowa kwa anthu, akuphunzira ace sanamloleza.