Acts 2:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuŵa sadaledzere ai, monga mukuganizira inu, pakuti nthaŵi idakali 9 koloko m'maŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti awa sanaledzera monga muyesa inu; pakuti ndi ora lachitatu lokha la tsiku;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunena zoona, anthu awa sanaledzere ayi, monga momwe mukuganizira, pakuti ino ndi 9 koloko mmawa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti awa sanaledzera monga muyesa inu; pakuti ndi ora lacitatulokha la tsiku;