Acts 2:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma zimenezi ndi zomwe mneneri Yowele adalosa kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
komatu ichi ndi chimene chinanenedwa ndi mneneri Yowele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma izi ndi zimene ananena Mneneri Yoweli kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
komatu ici ndi cimene cinanenedwa ndi mneneri Yoeli,