Acts 2:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Paja Davide ponena za Iye adati, ‘Ndinkaona Ambuye Mulungu pamaso panga nthaŵi zonse, pakuti amakhala ku dzanja langa lamanja kuti ndingagwedezeke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Davide anena za Iye, Ndinaona Mbuye pamaso panga nthawi zonse; chifukwa ali pa dzanja langa lamanja, kuti ndingasinthike;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Davide ananena za Iye kuti, “ ‘Ndinaona Ambuye pamaso panga nthawi zonse. Chifukwa Iye ali kudzanja langa lamanja, Ine sindidzagwedezeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Davine anena za Iye, Ndinaona Mbuye pamaso panga nthawi zonse; Cifukwa ali pa dzanja langa lamanja, kuti ndingasinthike;