Acts 2:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndikhulupirira kuti simudzandisiya ku Malo a anthu akufa, kapena kulekerera Woyera wanu kuti aole.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti simudzasiya moyo wanga ku dziko la akufa, kapena simudzapereka Woyera wanu aone chivunde,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa simudzasiya moyo wanga kumalo a anthu akufa, ku manda, kapena kulekerera Woyerayo kuti awole.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti simudzasiya moyo wanga ku Hade, Kapena simudzapereka Woyera wanu aone cibvunde,