Acts 2:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye kuti Davideyo adaaoneratu zimenezi, zakuti Khristu adzauka kwa akufa, ndipo pamenepo adanena mau aja akuti, “ ‘Iye sadasiyidwe ku Malo a anthu akufa, ndipo thupi lake silidaole.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iye pakuona ichi kale, analankhula za kuuka kwa Khristu, kuti sanasiyidwa m'dziko la akufa, ndipo thupi lake silinaona chivunde.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide ataoneratu zimene zinali mʼtsogolo anayankhula za kuuka kwa Khristu, kuti Iye sanasiyidwe mʼmanda, ndipo thupi lake silinawole.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iye pakuona ici kale, analankhula za kuuka kwa Kristu, kuti sanasiyidwa m'Hade, ndipo thupi lace silinaona cibvunde.