Acts 2:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu Davide sadakwere kupita Kumwamba, koma iye yemwe adati, “ ‘Ambuye adauza Mbuye wanga kuti, Khala ku dzanja langa lamanja
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Davide sanakwera Kumwamba ai; koma anena yekha, Ambuye anati kwa Mbuye wanga, khalani kudzanja lamanja langa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti si Davide anakwera kumwamba koma iye akuti, “ ‘Ambuye anawuza Ambuye anga kuti: Khala kudzanja langa lamanja
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Davine sanakwera Kumwamba ai; koma anena yekha, Ambuye anati kwa Mbuye wanga, Khalani ku dzanja lamanja langa,