Acts 20:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu aja adatenga mnyamata uja ali moyo, ndipo onse adasangalala kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza naye mnyamata ali wamoyo, natonthozedwa kwakukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu anatenga mnyamatayo kupita kwawo ali moyo ndipo anatonthozedwa mtima kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza naye mnyamata ali wamoyo, natonthozedwa kwakukuru.