Acts 20:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ndikukuuzani monenetsa lero, kuti ngati ena mwa inu atayike, izo nzao, ine ndilibepo mlandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndikuchitirani umboni lero lomwe, kuti ndilibe kanthu ndi mwazi wa anthu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chake, ine ndikukuwuzani lero kuti ndilibe mlandu ndi munthu aliyense.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndikucitirani umboni lero lomwe, kuti ndiribe kanthu ndi mwazi wa anthu onse.