Acts 20:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo adalira kwambiri. Adamkumbatira Pauloyo namumpsompsona polaŵirana naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo onsewa analira kwambiri, namkupatira Paulo pakhosi pake, nampsompsona,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse analira pamene amamukumbatira ndi kupsompsona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo onsewa analira kwambiri, namkupatira Paulo pakhosi pace, nampsompsona,