Acts 20:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamperekeza ndi Sopatere, mwana wa Piro, wa ku Berea; Aristariko ndi Sekundo a ku Tesalonika; Gayo wa ku Deribe; Timoteo; ndi Tikiko ndi Trofimo a ku Asiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamperekeza kufikira ku Asiya Sopatere mwana wa Piro, wa ku Berea; ndipo a Atesalonika, Aristariko ndi Sekundo; ndi Gayo wa ku Deribe, ndi Timoteo; ndi a ku Asiya, Tikiko ndi Trofimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapita pamodzi ndi Sopatro mwana wa Puro wa ku Bereya, Aristariko ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Derbe ndi Timoteyo, ndipo a ku Asiya anali Tukiko ndi Trofimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamperekeza kufikira ku Asiya Sopatro mwana wa Puro, wa ku Bereya; ndipo Atesalonika, Aristarko ndi Sekundo; ndi Gayo wa ku Derbe, ndi Timoteo; ndi a ku Asiya, Tukiko ndi Trofimo.