Acts 21:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake Paulo adatitenga kupita kwa Yakobe. Akuluampingo onse anali kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mawa mwake Paulo analowa nafe kwa Yakobo; ndi akulu onse anali pomwepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake Paulo pamodzi ndi ife tonse tinapita kwa Yakobo, ndipo akulu onse a mpingo anali komweko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mawa mwace Paulo analowa nafe kwa Yakobo; ndi akulu onse anali pomwepo.