Acts 21:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atalonjerana nawo, Paulo adaŵafotokozera mwatsatanetsatane zonse zimene Mulungu adaachita pakati pa anthu a mitundu ina kudzera mu utumiki wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atawalonjera iwo, anawafotokozera chimodzichimodzi zimene Mulungu anachita kwa amitundu mwa utumiki wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo anawalonjera ndi kuwafotokozera mwatsatanetsatane zimene Mulungu anachita pakati pa anthu a mitundu ina kudzera mu utumiki wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atawalankhula iwo, anawafotokozera cimodzi cimodzi zimene Mulungu anacita kwa amitundu mwa utumiki wace.