Acts 21:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye inu, muchite zimene tikuuzeni ife. Tili ndi amuna anai pano amene adachita lumbiro kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake uchite ichi tikuuza iwe; tili nao amuna anai amene anawinda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
tsono iwe chita zimene ife tikuwuze. Tili nawo amuna anayi pano amene anachita lumbiro kwa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ucite ici tikuuza iwe; tiri nao amuna anai amene anawinda;