Acts 21:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanena zimenezi chifukwa anali ataona Trofimo wa ku Efeso ali ndi Paulo mumzindamo, ndiye iwo ankaganiza kuti Paulo ndiye adaamloŵetsa m'Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti adaona Trofimo wa ku Efeso kale pamodzi ndi iye mumzinda; ameneyo anayesa kuti Paulo anamtenga nalowa naye ku Kachisi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ananena izi chifukwa anali ataona Trofimo wa ku Efeso ali ndi Paulo mu mzindamo ndipo iwo ankaganiza kuti Paulo anamulowetsa mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti adaona Trofimo wa ku Efeso kale pamodzi ndi iye mumzinda; ameneyo anayesa kuti Paulo anamtenga nalowa naye kuKacisi.