Acts 21:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidaona chilumba cha Kipro, koma tidachisiya ku dzanja lamanzere nkupita ku Siriya. Tidakafika ku Tiro, popeza kuti chombo chinkayenera kukatsitsa katundu kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene tinafika popenyana ndi Kipro, tinachisiya kulamanzere, nkupita ku Siriya; ndipo tinakocheza ku Tiro; pakuti pamenepo ngalawa inafuna kutula akatundu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tinaona chilumba cha Kupro ndipo tinadutsa kummwera kwake nʼkupita ku Siriya. Tinakayima ku Turo chifukwa sitima yathuyo imayenera kusiya katundu kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene tinafika popenyana ndi Kupro, tinacisiya kulamanzere, ntinapita ku Suriya; ndipo tinakoceza ku Turo; pakuti pamenepo ngalawainafuna kutula akatundu ace.