Acts 21:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu aja ankafuna kupha Paulo, mkulu wa gulu lonse la asilikali achiroma adalandira mau akuti mu mzinda wonse wa Yerusalemu muli chipolowe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene anafuna kumupha iye, wina anamuuza kapitao wamkulu wa gululo kuti m'Yerusalemu monse muli piringupiringu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anthuwo ankafuna kupha Paulo, nkhaniyi inamveka kwa mkulu wa magulu a asilikali a Aroma kuti mzinda wonse wa Yerusalemu wasokonezeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene anafuna kumupha iye, wina anamuuza kapitao wamkuru wa gululo kuti m'Yerusalemumonse muli pinngu-piringu,