Acts 21:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pamene adafika pa makwerero a kulingako, asilikali aja adachita kumnyamula, chifukwa chakuti anthuwo adaalusa zedi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anafika pamakwerero, kudatero kuti anamsenza asilikali chifukwa cha kulimbalimba kwa khamulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo atafika pa makwerero olowera ku malo a asilikaliwo, ananyamulidwa ndi asilikali chifukwa cha ukali wa anthuwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anafika pamakwerero, kudatero kuti anamsenza asilikari cifukwa ca kulimbalimba kwa khamulo;