Acts 21:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo ankaŵatsatira akufuula kuti, “Mupheni basi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti unyinji wa anthu unatsata, nufuula, Mchotse iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu la anthu limene linamutsatira linapitiriza kufuwula kuti, “Ameneyo aphedwe basi!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti unyinji wa anthu unatsata, nupfuula, Mcotse iye.