Acts 22:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindidathe kupenyanso chifukwa cha kuŵala kwakukulu kuja, nchifukwa chake anzanga aja adachita kundigwira pa dzanja nkumanditsogolera mpaka kukaloŵa m'Damasiko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo popeza sindinapenya, chifukwa cha ulemerero wa kuunikako, anandigwira dzanja iwo amene anali ndi ine, ndipo ndinafika ku Damasiko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anzanga anandigwira dzanja kupita nane ku Damasiko, popeza kuwala kunja kunandichititsa khungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo popeza sindinapenya, cifukwa ca ulemerero wa kuunikako, anandigwira dzanja iwo amene anali ndi ine, ndipo ndinafika ku Damasiko.