Acts 22:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kumeneko kunali munthu wina, dzina lake Ananiya. Anali munthu woopa Mulungu ndi wosamala Malamulo athu, ndipo Ayuda onse akumeneko ankamutama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu dzina lake Ananiya, ndiye munthu wopembedza monga mwa chilamulo, amene amchitira umboni wabwino Ayuda onse akukhalako,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munthu wina dzina lake Hananiya anabwera kudzandiona. Iyeyu anali munthu woopa Mulungu ndi wosunga Malamulo. Ayuda onse okhala kumeneko amamupatsa ulemu waukulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthu dzina lace Hananiya, ndiye munthu wopembedza monga mwa cilamulo, amene amcitira umboni wabwino Ayuda onse akukhalako,