Acts 22:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti udzamchitira umboni kwa anthu onse pa zimene waziwona ndi kuzimva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo udzamkhalira Iye mboni kwa anthu onse, za izo udaziona ndi kuzimva.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe udzakhala mboni yake kwa anthu onse pa zimene waziona ndi kuzimva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo udzamkhalira iye mboni kwa anthu onse, za izo udaziona ndi kuzimva.