Acts 22:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mtsogoleriyo adamva zimenezi, adapita kwa mkulu wa asilikali uja namufunsa kuti, “Kodi inu mukuti mutani? Munthu ujatu ndi mfulu yachiroma.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakumva ichi kenturiyoyo, ananka kwa kapitao wamkulu, namuuza, nanena, Nchiyani ichi uti uchite? Pakuti munthuyo ndiye Mroma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wolamulira asilikali 100 uja atamva zimenezi, anapita kwa mkulu wa asilikali ndi kumufotokozera. Iye anafunsa kuti, “Kodi mukuchita chiyani ndi munthuyu amene ndi nzika ya Chiroma?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakumva ici kenturiyoyo, ananka kwa kapitao wamkuru, namuuza, nanena, Nciani ici uti ucite? pakuti munthuyo ndiye Mroma.