Acts 22:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidagwa pansi kenaka ndidamva mau onena kuti, ‘Saulo, Saulo, ukundizunziranji?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinagwa pansitu, ndipo ndinamva mau akunena nane, Saulo, Saulo, undilondalonderanji Ine?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinagwa pansi ndipo ndinamva mawu akuti, ‘Saulo! Saulo! Ukundizunziranji?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinagwapansitu, ndipondinamva mau akunena nane, Saulo, Saulo, undilonda-londeranii Ine?