Acts 23:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kutacha, Ayuda ena adakhala upo, ndipo adapangana molumbira kuti, “Ife sitidya kapena kumwa chilichonse mpaka titamupha Pauloyo basi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kutacha, Ayuda anapangana chiwembu, nadzitemberera, ndi kunena kuti sadzadya kapena kumwa kanthu, kufikira atamupha Paulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kutacha Ayuda ena anakonza chiwembu ndipo analumbira kuti sadya kapena kumwa mpaka atapha Paulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kutaca, Ayuda anapangana ciwembu, nadzitemberera, ndi kunena kuti sadzadya kapena kumwa kanthu, kufikira atamupha Paulo;