Acts 23:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene adaapangana za chiwembu chimenechi analipo opititira makumi anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo iwo amene adachita chilumbiro ichi anali oposa makumi anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amene anakonza chiwembuchi analipo makumi anayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo iwo amene adacita cilumbiro ici anali oposa makumi anai.