Acts 23:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo adapita kwa akulu a ansembe ndi kwa akulu a Ayuda nakaŵauza kuti, “Ife talumbira kolimba kuti sitilaŵa kanthu mpaka titamupha Pauloyu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amenewo anadza kwa ansembe aakulu ndi akulu, nati, Tadzitemberera nalo temberero kuti sitidzalawa kanthu kufikira titamupha Paulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapita kwa akulu a ansembe ndi akuluakulu a Ayuda nakawawuza kuti, “Ife talumbira kolimba kuti sitidya kalikonse mpaka titapha Paulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amenewo anadza kwa ansembe akulu ndi akulu, nati, Tadzitemberera nalo temberero kuti sitidzalawa kanthu kufikira titamupha Paulo.