Acts 23:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mwana wa mlongo wake wa Paulo atamva za chiwembuchi, adakaloŵa m'linga la asilikali lija nakamtsina khutu Paulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mwana wa mlongo wake wa Paulo anamva za chifwamba chao, ndipo anadza nalowa m'linga, namfotokozera Paulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mwana wa mlongo wake wa Paulo atamva za chiwembuchi, anapita ku malo a asilikali aja namufotokozera Paulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mwana wa mlongo wace wa Paulo anamva za cifwamba cao, ndipo anadza nalowa m'linga, namfotokozera Paulo.