Acts 23:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Paulo adaitana mmodzi mwa atsogoleri a asilikali namuuza kuti, “Tapitani ndi mnyamatayu kwa mkulu wa asilikali, akuti ali naye ndi mau.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Paulo anadziitanira kenturiyo wina, nati, Pita naye mnyamata uyu kwa kapitao wamkulu; pakuti ali nako kanthu kakumfotokozera iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo anayitana mmodzi wa wolamulira asilikali 100 aja, namuwuza kuti, “Pita naye mnyamatayu kwa mkulu wa asilikali. Iyeyu ali ndi mawu oti akamuwuze.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Paulo anadziitanira kenturiyo wina, nati, Pita naye mnyamata uyu kwa kapitao wamkuru; pakuti ali nako kanthu kakumfotokozera iye.