Acts 23:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Ananiya, mkulu wa ansembe onse, adalamula amene adaaimirira pafupi ndi Paulo kuti, “Mtchayeni kukamwako!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkulu wa ansembe Ananiya analamulira akuimirirako ampande pakamwa pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha mawu amenewa, mkulu wa ansembe Ananiya analamulira amene anali pafupi ndi Paulo kuti amumenye pakamwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkulu wa ansembe Hananiya analamulira akuimirirako ampande pakamwa pace.