Acts 23:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mkulu wa asilikali uja adauza mnyamatayo kuti, “Chabwino, iwe pita, koma usaululire wina aliyense kuti wadzandifotokozera zimenezi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndipo kapitao wamkulu anauza mnyamatayo apite, namlamulira kuti, Usauze munthu yense kuti wandizindikiritsa izi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkulu wa asilikaliyo anawuza mnyamatayo kuti apite koma anamuchenjeza kuti, “Usawuze munthu aliyense kuti wandifotokozera zimenezi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndipo kapitao wamkuru anauza mnyamatayo apite, namlamulira kuti, Usauze munthu yense kuti wandizindikiritsa izi.