Acts 23:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ine Klaudio Lisiasi, ndikupereka moni kwa inu olemekezeka, a Felikisi, bwanamkubwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Klaudio Lisiasi kwa kazembe womveketsa Felikisi, ndikupatsani moni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine Klaudiyo Lusiya, Kwa wolemekezeka, bwanamkubwa Felike: Ndikupereka moni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Klaudiyo Lusiya kwa kazembe womveketsa Felike, ndikulankhulani.