Acts 23:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkafuna kudziŵa chifukwa chimene ankamunenezera, choncho ndidapita naye ku Bwalo lao Lalikulu lamilandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pofuna kuzindikira chifukwa chakuti anamnenera iye, ndinatsikira naye ku bwalo la akulu ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinkafuna kudziwa mlandu umene anapalamula, choncho ndinapita naye ku Bwalo lawo Lalikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pofuna kuzindikira cifukwa cakuti anamnenera iye, ndinatsikira naye ku bwalo la akuru ao.