Acts 23:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake iwo adabwerera ku linga la asilikali, nasiya okwera pa kavalo aja kuti apitirire ndi Paulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma m'mawa mwake anasiya apakavalo amperekeze, nabwera kulinga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake iwo anabwerera ku malo a asilikali nasiya okwera pa akavalo kuti apitirire ndi Paulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma m'mawa mwace anasiya apakavalo amperekeze, nabwera kulinga;