Acts 23:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo aja atafika ku Kesareya, adapereka kalata ija kwa bwanamkubwa, naperekanso Paulo m'manja mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iwowo, m'mene anafika ku Kesareya, anapereka kalata kwa kazembe, naperekanso Paulo kwa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asilikali okwera pa akavalowo atafika ku Kaisareya anapereka kalatayo kwa bwanamkubwa, namuperekanso Paulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iwowo, m'mene anafika ku Kaisareya, anapereka kalata kwa kazembe, naperekanso Paulo kwa iye.