Acts 23:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwanamkubwa uja ataŵerenga kalatayo, adafunsa Paulo za dera kumene ankachokera. Pamene adamva kuti ngwochokera ku Silisiya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene adawerenga anafunsa achokera m'dziko liti; ndipo pozindikira kuti anali wa ku Silisiya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwanamkubwayo anawerenga kalatayo ndipo anamufunsa Paulo za dera limene amachokera. Atazindikira kuti amachokera ku Kilikiya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene adawerenga anafunsa acokera m'dziko liti; ndipo pozindikira kuti anali wa ku Kilikiya,