Acts 23:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paulo adati, “Pepani abale, sindimadziŵa kuti ndi mkulu wa ansembe onse. Paja mau a Mulungu akuti, ‘Usamnenere zoipa woweruza anthu ako.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Paulo anati, Sindinadziwa, abale, kuti ndiye mkulu wa ansembe; pakuti kwalembedwa, Usamnenera choipa mkulu wa anthu ako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo anayankha nati, “Abale, ine sindinazindikire kuti ndi mkulu wa ansembe; pakuti kunalembedwa kuti, ‘Usayankhule zoyipa kwa mtsogoleri wa anthu ako.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Paulo anati, Sindinadziwa, abale, kuti ndiye mkulu wa ansembe; pakuti kwalembedwa, Usamnenera coipa mkulu wa anthu ako.