Acts 24:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popeza kuti ndimakhulupirira Mulungu, ndimakhulupirira, monga iwonso amakhulupirira, kuti anthu onse, olungama ndi osalungama omwe, adzauka kwa akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kukhala nacho chiyembekezo cha kwa Mulungu chimene iwo okhanso achilandira, kuti kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndili nacho chiyembekezo chomwecho chimene iwo ali nacho mwa Mulungu, kuti kudzakhala kuuka kwa akufa kwa olungama ndiponso kwa ochimwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kukhala naco ciyembekezo ca kwa Mulungu cimene iwo okhanso acilandira, kuti kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama.