Acts 24:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono nditakhala kwina zaka zingapo, ndidabwera kudzatula zopereka zachifundo kwa anthu a mtundu wanga, ndiponso kudzapereka nsembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zitapita zaka zambiri ndinadza kutengera mtundu wanga zachifundo, ndi zopereka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Patapita zaka zambiri, ndinabwera ku Yerusalemu kudzapereka mphatso kwa anthu osauka a mtundu wanga komanso kudzapereka nsembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zitapita zaka zambiri ndinadza kutengera mtundu wanga zacifundo, ndi zopereka;