Acts 24:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndinkachita zimenezi, iwo adandipeza m'Nyumba ya Mulungu nditachita mwambo wakudziyeretsa. Panalibe konse khamu la anthu kapena chipolowe ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popereka izi anandipeza woyeretsedwa m'Kachisi, wopanda khamu la anthu, kapena phokoso;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndinkachita zimenezi, iwo anandipeza mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu nditachita mwambo wodziyeretsa. Panalibe gulu la anthu kapena kuti ndimachita za chisokonezo chilichonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
popereka izi anandipeza woyeretsedwa m'Kacisi, wopanda khamu la anthu, kapena phokoso; koma panali Ayuda ena a ku Asiya,