Acts 24:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kunali Ayuda ena a ku Asiya. Iwowo akadayenera kukhala pano pamaso panu kudzandineneza okha ngati ali nane nkanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma panali Ayuda ena a ku Asiya, ndiwo mwenzi atakhala pano pamaso panu ndi kundinenera, ngati ali nako kanthu kotsutsa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pali Ayuda ena ochokera ku Asiya, amene amayenera kukhala pano pamaso panu, kundiyimba mlandu ngati ali ndi kalikonse konditsutsa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiwo mwenzi atakhala pano pamaso panu ndi kundinenera, ngati ali nako kanthu kotsutsa ine.