Acts 24:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma cholakwa changa chingathe kukhala chokhachi chakuti, pamene ndidaaimirira pamaso pao, ndidaafuula kuti, ‘Mukundizenga mlandu ine lero chifukwa ndimakhulupirira kuti anthu akufa adzauka.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma mau awa amodzi okha, amene ndinafuula poimirira pakati pao, Kunena za kuuka kwa akufa ndiweruzidwa ndi inu lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma cholakwa changa chingathe kukhala chokhachi chakuti, nditayima pamaso pawo ndinafuwula kuti, ‘Mukundiweruza ine lero chifukwa ndimakhulupirira kuti akufa adzauka.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma mau awa amodzi okha, amene ndinapfuula poimirira pakati pao, Kunena za kuuka kwa akufa ndiweruzidwa ndi inu lero lino.