Acts 24:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adalamula mtsogoleri wa gulu la asilikali kuti azimlonda, koma azimpatsakonso ufulu, osaletsa abwenzi ake kumamsamala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analamulira kenturiyo amsunge iye, koma akhale nao ufulu, ndipo asaletse anthu ake kumtumikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye analamulira woyangʼanira asilikali 100 kuti alondere Paulo, koma azimupatsako ufulu ndiponso kulola abwenzi ake kuti adzimusamalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analamulira kenturiyo amsunge iye, koma akhale nao ufulu, ndipo asaletse anthu ace kumtumikira.