Acts 24:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita zaka ziŵiri, Porkio Fesito adaloŵa m'malo mwa Felikisi. Tsono Felikisiyo pofuna kuchita mkomya kwa Ayuda, adamsiya m'ndende Paulo uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma zitapita zaka ziwiri Porkio Fesito analowa m'malo a Felikisi; ndipo Felikisi pofuna kukonda Ayuda anamsiya Paulo m'nsinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita zaka ziwiri, Porkiyo Festo analowa mʼmalo mwa Felike, koma anamusiya Paulo mʼndende, chifukwa amafuna kuti Ayuda amukonde.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma zitapita zaka ziwiri Porkiyo Festo analowa m'malo a Felike; ndipo Felike pofuna kukonda Ayuda anamsiya Paulo m'nsinga.