Acts 24:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pepani sindikufuna kukutayitsani nthaŵi, komabe ndimapempha kuti mundikomere mtima, mungomvapo mau athuŵa mwachidule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kuti ndingaonjeze kukulemetsani ndikupemphani mutimvere mwachidule ndi chifatso chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kuti tisakuchedwetseni, ndikupempha kuti mwa kuleza mtima kwanu mutimvere ife.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kuti ndingaonjeze kukulemetsani ndikupempha, ni mutimvere mwacidule ndi cifatso canu.