Acts 25:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Fesito adayamba ntchito yoweruza m'chigawo chake, ndipo patapita masiku atatu, adapita ku Yerusalemu kuchokera ku Kesareya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Fesito m'mene analowa dziko lake, ndipo atapita masiku atatu, anakwera kunka ku Yerusalemu kuchokera ku Kesareya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita masiku atatu Festo atafika mʼdera lake, anachoka ku Kaisareya ndi kupita ku Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Festo m'mene analowa dziko lace, ndipo atapita masiku atatu, anakwera kunka ku Yerusalemu kucokera ku Kaisareya.